1 Corinthians 14:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muziyesetsa kukhala nacho chikondi, komanso muike mtima pa mphatso zimene Mzimu Woyera amapereka, makamaka mphatso ya kulankhula mau ochokera kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsatani chikondi; koma funitsitsani mphatso zauzimu, koma koposa kuti mukanenere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Funafunani chikondi, ndikufunitsitsa mphatso zauzimu, makamaka mphatso ya uneneri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsatani cikondi; koma funitsitsani mphatsozauzimu, koma koposa kuti mukanenere.