1 Corinthians 14:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuthokoza Mulungu kuti ine ndimalankhula m'zilankhulo zosadziŵika kuposa nonsenu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiyamika Mulungu kuti ndilankhula malilime koposa inu nonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikuyamika Mulungu chifukwa ndimayankhula malilime kuposa nonsenu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiyanillca Mulungu kuti ndilankhula malilime koposa inu nonse;