1 Corinthians 14:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga nkuti mau a Mulungu adachokera kwa inu? Kaya kapena adafika kwa inu nokha?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mau a Mulungu anatuluka kwa inu? Kapena anafika kwa inu nokha?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi kapena mawu a Mulungu anachokera kwa inu? Kapena anafika kwa inu nokha?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mau a Mulungu anatutuka kwa iw? kapena anafika kwa inu nokha?