1 Corinthians 15:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati akufa sadzauka, ndiye kuti Khristunso sadauke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati kulibe kuuka kwa akufa, Khristunso sanaukitsidwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati kulibe kuuka kwa akufa, ndiye kuti ngakhale Khristu sanaukenso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati kulibe kuuka kwa akufa, Kristunso sanaukitsidwa;