1 Corinthians 15:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ngati Khristu sadauke, kulalika kwathu nkwachabe, ndipo chikhulupiriro chanu nchachabenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ngati Khristu sanaukitsidwa kulalikira kwathu kuli chabe, chikhulupiriro chanunso chili chabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati Khristu sanaukitsidwe, ndiye kuti kulalikira kwathu nʼkopanda ntchito, ndipo chikhulupiriro chanu nʼchopandanso ntchito.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ngati Kristu sanaukitsidwakulalikira kwathu kuli cabe, cikhulupiriro canunso ciri cabe.