1 Corinthians 15:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo nawonso amene adamwalira ali okhulupirira Khristu, adatayika ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake iwonso akugona mwa Khristu anatayika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiye kuti nawonso amene agona tulo mwa Ambuye ndi otayika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace iwonso akugona mwa Kristu anatayika.