1 Corinthians 15:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati taika chikhulupiriro chathu mwa Khristu chifukwa cha moyo uno wokha, ndiye kuti ndife omvetsa chisoni koposa anthu ena onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati tiyembekezera Khristu m'moyo uno wokha, tili ife aumphawi oposa a anthu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati kukanakhala kuti tili ndi chiyembekezo mwa Khristu mʼmoyo uno wokha, tikanakhala omvetsa chisoni kuposa anthu ena onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati tiyembekezera Kristu m'moyo uno wokha, tiri ife aumphawi oposa a anthu onse,