1 Corinthians 15:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ai, Khristu adauka ndithu kwa akufa. Pakati pa onse amene adafa, ndiye woyamba kuuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa, chipatso choundukula cha iwo akugona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nʼzoonadi kuti Khristu anaukitsidwa kwa kufa, chipatso choyamba cha onse ogona tulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsopano Kristu waukitsidwa kwa akufa, cipatso coundukula ca iwo akugona.