1 Corinthians 15:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Khristu ayenera kulamulira mpaka atagonjetsa adani ake onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ayenera kuchita ufumu kufikira ataika adani onse pansi pa mapazi ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Iye ayenera kulamulira mpaka Mulungu atayika pansi pa mapazi ake adani ake onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ayenera kucita ufumu kufikira ataika adani onse pansi pa mapazi ace.