1 Corinthians 15:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kapena wina nkufunsa kuti, “Kodi akufa adzauka bwanji? Kodi adzakhala ndi thupi lotani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wina adzati, Akufa aukitsidwa bwanji? Ndipo adza nalo thupi lotani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma wina akhoza kufunsa kuti, “Kodi akufa amaukitsidwa motani? Adzauka ndi thupi la mtundu wanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wina adzati, 7 Akufa aukitsidwa bwanji? Ndipo adza nalorhupi lotani?