1 Corinthians 15:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaikidwa m'manda, mkucha wake adauka, monga Malembo anenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti anaikidwa; ndi kuti anaukitsidwa tsiku lachitatu, monga mwa malembo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti anayikidwa mʼmanda, kuti anaukitsidwa tsiku lachitatu monga mwa Malemba;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti anaikidwa; ndi kutianaukitsidwa tsiku lacitatu, monga mwa malembo;