1 Corinthians 15:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palinso zolengedwa zakuthambo, ndi zina zapansipano. Koma ulemerero wa zakuthambo ndi wosiyana ndi ulemerero wa zapansipano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Palinso matupi am'mwamba, ndi matupi apadziko: koma ulemerero wa lam'mwamba ndi wina, ndi ulemerero wa lapadziko ndi winanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palinso matupi akumwamba ndipo palinso matupi a dziko lapansi; koma ulemerero wa matupi akumwamba ndi wina, ndi wa matupi a dziko lapansi ndi winanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Palinso matupi am'mwamba, ndi matupi apadziko: koma ulemerero wa lam'mwamba ndi wina, ndi ulemerero wa lapadziko ndi winanso.