1 Corinthians 15:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamu woyamba uja anali wochokera ku dothi, anali wapansipano. Koma Khristu, Adamu wachiŵiri uja, anali wochokera Kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu woyambayo ali wapansi, wanthaka. Munthu wachiwiri ali wakumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu woyamba anali wa dziko lapansi, wochokera mʼnthaka koma munthu wachiwiri anali wochokera kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
13 Munthu woyambayo ali wapansi, wanthaka. Munthu waciwiri ali wakumwamba.