1 Corinthians 15:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse apansipano ali ngati Adamu wopangidwa ndi dothi uja. Ndipo onse amene ali a Kumwamba, ali ngati Khristu wa Kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga wanthakayo, ateronso anthaka; ndi monga wakumwamba, ateronso akumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga analili munthu wa dziko lapansi, momwemonso anthu onse amene ndi a dziko lapansi. Ndipo monga alili munthu wakumwamba, momwemonso anthu onse amene ndi akumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
14 Monga wanthakayo, ateronso anthaka; ndi monga wakumwamba, ateronso akumwamba.