1 Corinthians 15:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga takhala ofanafana ndi Adamu, munthu wopangidwa ndi dothi uja, momwemonso tidzakhala ofanafana ndi Khristu, munthu wa Kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo monga tavala fanizo la wanthakayo, tidzavalanso fanizo la wakumwambayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo monga momwe tinabadwa ofanana ndi munthu wa dziko lapansi uja, momwemonso tidzakhala ofanana ndi munthu wakumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 15 monga tabvaia fanizo la wanthakayo, tidzabvalanso fanizo la wakumwambayo.