1 Corinthians 15:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adaonekera abale opitirira mazana asanu pa nthaŵi imodzi. Ambiri mwa iwowo akalipo, ena adamwalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pomwepo anaoneka pa nthawi imodzi kwa abale oposa mazana asanu, amene ochuluka a iwo akhala kufikira tsopano, koma ena agona;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake, Iye anaonekera kwa anthu oposa 500 mwa abale pa nthawi imodzi, ndipo ambiri mwa iwo akanali ndi moyo ngakhale kuti ena anagona tulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pomwepo anaoneka pa nthawi imodzi kwa abale oposa mazana asanu, amene ocuruka a iwo akhala kufikira tsopano, koma ena agona;