1 Corinthians 15:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adaonekera Yakobe, kenaka atumwi onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pomwepo anaonekera kwa Yakobo; pamenepo kwa atumwi onse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anaonekeranso kwa Yakobo, kenaka kwa atumwi onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pomwepoanaonekera kwa Yakobo; pamenepo kwa: atumwi onse;