1 Corinthians 16:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndakondwa kuti Stefanasi, Fortunato ndi Akaiko afika, pakuti ngakhale inu simuli nane, iwo achita ngati kuloŵa m'malo wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndikondwera pa kudza kwao kwa Stefanasi, ndi Fortunato, ndi Akaiko; chifukwa iwo anandikwaniritsa chotsalira chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikondwera kuti Stefano, Fortunato ndi Akayiko afika, chifukwa akhala akundithandiza pakuti inu simuli nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndikondwera pa kudza kwao kwa Stefana, ndi Fortunato, ndi Akayiko; cifukwa iwo anandikwaniritsa cotsalira canu.