1 Corinthians 16:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandisangulutsa ine monga adasangulutsanso inu. Anthu otere muziŵalemekeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anatsitsimutsa mzimu wanga ndi wanu; chifukwa chake muzindikire otere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti anatsitsimutsa mzimu wanga ndi wanu womwe. Anthu a mtundu oterewa ngofunika kuwalemekeza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anatsitsimutsa mzimu wanga ndi wanu; cifukwa cace muzindikire otere.