1 Corinthians 16:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mipingo ya ku dziko la Asiya ikuti moni. Akwila ndi Prisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m'nyumba mwao, akuti moni kwa inu nonse, akhristu anzao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mipingo ya ku Asiya ikupatsani moni. Akupatsani moni ndithu inu mwa Ambuye, Akwila ndi Prisika, pamodzi ndi Mpingo wa m'nyumba yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpingo wa mʼchigawo cha ku Asiya ukupereka moni. Akula ndi Prisila akuperekanso moni wachisangalalo, mwa Ambuye, ndiponso mpingo umene umakumana mʼnyumba mwawo ukupereka moni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mipingo ya ku Asiya ilankhula inu. Akulankhulani ndithu inu mwa Ambuye, Akula ndi Priska, pamodzi ndi Mpingo wa m'nyumba yao,