1 Corinthians 16:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kapena kwanuko ndidzakhala kanthaŵi, kapenanso nyengo yonse yachisanu. Ndifuna kuti pambuyo pake mudzandithandize kupitiriza ulendo wanga kulikonse kumene ndingapite.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo kapena ndidzakhalitsa ndi inu, kapenanso kugonera nyengo yachisanu kuti mukandiperekeze ine kumene kulikonse ndipitako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwina ndidzakhala nanu kanthawi kochepa kapenanso nyengo yonse yozizira, kuti mudzandithandize kupitiriza ulendo wanga kulikonse kumene ndingapite.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo kapena ndidzakhalitsa ndi inu, kapenanso kugonera nyengo yacisanu kuti mukandiperekeze ine kumene kuli konse ndipitako,