1 Corinthians 16:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti pano mwai ulipo woti nkuchita zazikulu, ndiponsotu adani alipo ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti panditsegukira pa khomo lalikulu ndi lochititsa, ndipo oletsana nafe ndi ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti mwayi waukulu wapezeka woti nʼkugwira ntchito yaphindu, koma pali ambiri amene akutsutsana nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti panditsegukira pa khomo lalikuru ndi locititsa, ndipo oletsana nafe ndi ambiri.