1 Corinthians 3:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono musadzinyenge. Ngati wina mwa inu adziyesa wanzeru, kunena za nzeru za masiku ano, ameneyo ayambe wakhala ngati wopusa, kuti asanduke wanzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu asadzinyenge yekha; ngati wina ayesa kuti ali wanzeru mwa inu m'nthawi yino ya pansi pano, akhale wopusa, kuti akakhale wanzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho musadzinyenge. Ngati wina wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru pa mulingo wa mʼbado uno, ayenera kukhala “wopusa” kuti athe kukhala wanzeru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu asadzinyenge yekha; igati winaayesa kuti ali wanzeru nwa inu m'nthawi yino ya pansi iano, akhale wopusa, kuti akakhale vanzeru.