1 Corinthians 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakumwetsani mkaka, osakupatsani chakudya cholimba, chifukwa simukadatha kuchidya. Ngakhalenso tsopano simungathe kuchidya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinadyetsa inu mkaka, si chakudya cholimba ai; pakuti simunachikhoza; ngakhale tsopano lino simuchikhoza; pakuti mulinso athupi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinakupatsani mkaka osati chakudya cholimba pakuti munali musanakonzeke kuchilandira. Zoonadi, simunakonzekebe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinaiyetsa inu mkaka, si cakudya colimba ai; pakuti simunaeikhoza; ngakhale tsopano lino simucikhoza; pakuti mulinso athupi;