1 Corinthians 3:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Penanso Malembo akuti, “Ambuye amaŵadziŵa maganizo a anthu anzeru kuti ndi achabe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za anzeru, kuti zili zopanda pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso, “Ambuye amadziwa kuti maganizo a wanzeru ndi opandapake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za mzeru, kuti ziri zopanda pace.