1 Corinthians 3:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake pasakhale wina aliyense wonyadira anthu chabe. Zinthu zonse nzanu:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake palibe mmodzi adzitamande mwa anthu. Pakuti zinthu zonse nzanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho, wina asanyadire anthu chabe! Zonse ndi zanu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace palibemmodzi adziamande mwa anthu. Pakuti zinthu onse nzanu;