1 Corinthians 3:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero wobzala kapenanso wothirira sali kanthu, koma Mulungu yekha amene amameretsa, ndiye ali kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chotero sali kanthu kapena wookayo, kapena wothirirayo; koma Mulungu amene akulitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho kuphatikiza iye wodzala ndi iye wothirira, onse sali kanthu, koma Mulungu yekha amene amakulitsa zinthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cotero sali kanthu kapena wookayo, kapena wothirirayo; kama Mulungu amene akulitsa.