1 Corinthians 5:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi Mulungu amene amaweruza anthu akunjawo. Paja mau a Mulungu akuti, “Munthu woipayo mumchotse pakati panu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma akunja awaweruza Mulungu? Chotsani woipayo pakati pa inu nokha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu adzaweruza akunja. “Chotsani woyipayo pakati panu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
komaakunia awaweruza Mulungu? Cotsani woipayo pakati pa inu nokha.