1 Corinthians 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'kalata imene ndidaakulemberani, ndidaakuuzani kuti musamayanjane nawo anthu adama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinalembera inu m'kalata uja, kuti musayanjane ndi achigololo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakulemberani mʼkalata yanga kuti musayanjane nawo anthu achigololo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinalembera inu m'kalata uja, kuti musayanjane ndi acigololo;