1 Corinthians 6:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ngati muli ndi milandu pa zinthu zotere, bwanji mumaika anthu amene mpingo suŵayesa kanthu kuti aiweruze?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake, ngati muli nayo milandu ya zinthu za moyo uno, kodi muweruzitsa iwo amene ayesedwa achabe mu Mpingo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake, ngati pali milandu pa zinthu zotere, sankhani anthu ena kuti akhale oweruza ngakhale alibe udindo mu mpingo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace, ngati muli nayo mirandu ya zinthu za moyo uno, kodi muweruzitsa iwo amene ayesedwa acabe mu Mpingo?