1 Corinthians 7:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale, aliyense angokhala pamaso pa Mulungu monga momwe analiri pamene Mulunguyo adamuitana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yense, m'mene anaitanidwamo, abale, akhale momwemo ndi Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale, aliyense angokhala pamaso pa Mulungu monga momwe analili pamene Mulungu anamuyitana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yense, m'mene anaitanidwamo, abate, akhale momwemo ndi Mulungu.