1 Corinthians 7:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma munthu wokwatira amatekeseka ndi zapansipano, kuganiza za m'mene angakondweretsere mkazi wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma iye wokwatira alabadira zinthu za dziko lapansi, kuti akondweretse mkazi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma wa pa banja amalabadira za dziko lapansi lino, mmene angakondweretsere mkazi wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma iye wokwatira alabadira zinthu za dziko lapansi, kuti akondweretse mkazi wace.