1 Corinthians 7:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndikunena zimenezi, sindikuchita mokulamulani ai, koma mokulolani chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ichi ndinena monga mwa kulola, si monga mwa kulamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikunena zimenezi mokulolani chabe osati mokulamulani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ici ndinena monga mwa kulola, si monga mwa kulamulira.