1 Corinthians 8:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano ndifuna kunena za chakudya choperekedwa kwa mafano. Nzoonadi kuti tonse tili nazo nzeru, komatu nzeru zokha zimangotukumula anthu. Chikondi ndicho chimapindulitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma za zoperekedwa nsembe kwa mafano: Tidziwa kuti tili nacho chidziwitso tonse. Chidziwitso chitukumula, koma chikondi chimangirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano za chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano: Ife tidziwa kuti tonse tili ndi chidziwitso. Komatu chidziwitso chokha chimadzitukumula, koma chikondi ndicho chimapindulitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma za zoperekedwa nsembe kwa mafano: Tidziwa kuti tid naco cidziwitso tonse. Cidziwitso citukumula, koma cikondicimangirira.