1 Corinthians 8:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero amene chikhulupiriro chake nchosalimba kwenikweni, adzatayika chifukwa cha iwe amene uli wodziŵa. Chonsecho tsono iyeyo ndi mbale wako amene Khristu adamufera!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwa chidziwitso chako wofookayo atayika, ndiye mbale amene Khristu anamfera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero kuti chifukwa cha chidziwitso chanu mʼbale wofowokayu amene chifukwa cha iye, Khristu anafa, wawonongeka chifukwa cha chidziwitso chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwa cidziwitso cako wofokayo atayika, ndiye mbale amene Kristu anamfera.