1 Corinthians 8:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma munthu akamakonda Mulungu, ndiye kuti amadziŵika ndi Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati wina akonda Mulungu, yemweyu adziwika ndi Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma munthu amene amakonda Mulungu amadziwika ndi Mulunguyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati wina akonda Mulungu, yemweyu adziwika ndi iye.