1 Corinthians 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe chenjerani kuti ufulu wanuwu pochita zinthu, ungaphunthwitse ena amene chikhulupiriro chao nchosalimba kwenikweni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma yang'anirani kuti ulamuliro wanu umene ungakhale chokhumudwitsa ofookawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe samalani kuti ufulu wanu ochita zinthu usafike pokhumudwitsa ofowoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma yang'anirani kuti ulamuliro wanu umene ungakhale cokhumudwitsa ofokawo.