1 Corinthians 9:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ife tidafesa zabwino zauzimu pakati panu, nanga tilekerenji kulandira kwa inu zotisoŵa m'moyo wathu wathupi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati takufeserani inu zauzimu, kodi nchachikulu ngati ife tituta za thupi lanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati tidzala mbewu yauzimu pakati panu, kodi ndi chovuta kwambiri kuti tikolole zosowa zathu kuchokera kwa inu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati takufeserani inu zauzimu, kodi ncacikuru ngati ife tituta za thupi lanu?