1 Corinthians 9:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi simudziŵa kuti otumikira m'Nyumba ya Mulungu, amadya chakudya cha m'Nyumbamo, ndipo kuti opereka nsembe pa guwa lansembe, amalandira nao zansembezo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi simudziwa kuti iwo akutumikira za Kachisi amadya za m'Kachisi, ndi iwo akuimirira guwa la nsembe, agawana nalo guwa la nsembe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi simukudziwa kuti wogwira ntchito mʼNyumba ya Mulungu amapeza chakudya chawo mʼNyumbamo, ndipo kuti otumikira pa guwa lansembe amagawana zimene zaperekedwa pa guwa lansembelo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi simudziwa kuti iwo akutumikira za kacisi amadya za m'Kacisi, ndi iwo akuimirira guwa la nsembe, agawana nalo guwa la nsembe?