1 Corinthians 9:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene ndimaŵayankha ofufuza za ine ndi izi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chodzikanira changa kwa iwo amene andifunsa ine ndi ichi:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa iwo wofuna kundizenga milandu ndimawayankha kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Codzikanira canga kwa iwoamene andifunsa ine ndi ici: