1 Corinthians 9:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ine ndi Barnabasi, ndife tokha oyenera kugwira ntchito zamanja kuti tizidzipezera tokha zotisoŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena kodi ife tokha, Barnabasi ndi ine tilibe ulamuliro wakusagwira ntchito?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi kapena ine ndekha ndi Barnaba ndiye tikuyenera kugwira ntchito kuti tipeze zotisowa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena kodi ife tokha, Bamaba ndi ine, tiribe ulamuliro wakusagwira nchito?