1 John 2:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu ana, ndikukulemberani popeza kuti Mulungu wakukhululukirani machimo anu chifukwa cha dzina la Khristu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikulemberani, tiana, popeza machimo adakhululukidwa kwa inu mwa dzina lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu ana okondedwa, ndikukulemberani popeza kuti machimo anu akhululukidwa chifukwa cha dzina la Yesu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikulemberani, tiana, popeza macimo adakhululukidwa kwa inu mwa dzina lace.