1 John 2:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense wokana Mwana, alibenso Atate. Wovomereza Mwana, alinso ndi Atate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yense wakukana Mwana, alibe Atate; wovomereza Mwana ali ndi Atatenso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wokana Mwana alibenso Atate. Wovomereza Mwana alinso ndi Atate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
5 Yense wakukana Mwana, alibe Atate; wobvomereza Mwana ali ndi Atatenso.