1 John 2:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakutsata malamulo a Mulungu, ndi pamene tingatsimikize kuti timamdziŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo umo tizindikira kuti tamzindikira Iye, ngati tisunga malamulo ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife timatsimikiza kuti tikumudziwa ngati tikusunga malamulo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo umo tizindikira kuti tamzindikira iye, ngati tisunga malamulo ace.