1 John 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akamati, “Ine ndimadziŵa Mulungu”, koma chikhalirecho satsata malamulo ake, angonama ameneyo, ndipo mwa iye mulibe choona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye wakunena kuti, Ndimdziwa Iye, koma wosasunga malamulo ake, ali wabodza, ndipo mwa iye mulibe choonadi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu akamanena kuti, “Ine ndimadziwa Mulungu,” koma samvera malamulo a Mulunguyo, ndi wabodza ameneyo ndipo mwa iye mulibe choonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye wakunena kuti, Ndimdziwa iye, koma wosasunga malamulo ace, ali wabodza, ndipo mwa iye mulibe coonadi;