1 John 2:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akamati ali m'kuŵala, komabe nkumadana ndi mnzake, akali mu mdima ameneyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye amene anena kuti ali m'kuunika, namuda mbale wake, ali mumdima kufikira tsopano lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amene amati ali mʼkuwunika, koma nʼkumadana ndi mʼbale wake ali mu mdima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iye amene anena kuti ali m'kuunika, namuda mbale wace, ali mumdima kufikira tsopane lino.