1 John 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uthenga umene mudamva kuyambira pa chiyambi ndi wakuti tizikondana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti uwu ndi uthenga mudaumva kuyambira pachiyambi, kuti tikondane wina ndi mnzake:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga umene munawumva kuyambira pachiyambi ndi uwu: Tizikondana wina ndi mnzake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti uwu ndi uthenga mudaumva kuyambira paciyambi, kuti tikondane wina ndi mnzace: