1 John 3:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero musadabwe abale, anthu odalira zapansipano akamadana nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musazizwe, abale, likadana nanu dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale anga, musadabwe ngati dziko lapansi lidana nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musazizwe, abale, Jikadana nanu dziko lapansi.