1 John 4:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aneneri onamawo ndi apansipano, nchifukwa chake zimene amalankhula nzapansipano, ndipo anthu odalira zapansipano amaŵamvera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mwa ichi alankhula monga ochokera m'dziko lapansi, ndipo dziko lapansi liwamvera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aneneri onyengawa ndi ochokera mʼdziko lapansi, nʼchifukwa chake amayankhula za dziko lapansi, ndipo dziko lapansi limawamvera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mwa ici alankhula monga ocokera m'dziko lapansi, ndipo dziko tapansi liwamve ra.