1 John 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Timalandira umboni wa anthu, koma umboni wa Mulungu ndi wopambana umboni wa anthu. Umboniwo ndi umene Mulungu adachitira Mwana wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati tilandira umboni wa anthu, umboni wa Mulungu uposa; chifukwa umboni wa Mulungu ndi uwu, kuti anachita umboni za Mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Timalandira umboni wa anthu, koma umboni wa Mulungu ndi wopambana. Umboniwo ndi umene anachitira Mwana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati tilandira umboni wa anthu, umboni wa Mulungu uposa; cifukwa umboni wa Mulungu ndi uwu, kuti anacita umboni za Mwana wace.